CRUISE 5 WITH MOSE WA PA PHIRI LA BUNDA
Joab Frank Chakhaza Joab Frank Chakhaza
64.2K subscribers
112,054 views
774

 Published On Feb 22, 2021

Mose wa pa Phiri la Bunda (Radford Kamwendo) adakwela pa phiri kuti akapemphere, ali pomwepo adalandira ulosi kuchokela kwa ma Prophet kuti akuyenela kukhala pamwamba pomwepo kuti azisamalire malowo. Pano wakhala pa phiri lo kwa zaka zitatu.


Mose adakula moyo ovutika, kulekela sukulu pa Standard 8, kugwila ntchito ngati lebala, kenako ngati msilikali kwa zaka 6, kenako ngati truck driver. Mose ndiokwatila ndipo ali ndi ana akulu akulu. Atazindikila kuti akukhala moyo wosokonekela adaganiza zoyamba kusala komanso kupemphera. Ndipamene adakapezeka pamwamba pa phiri la Bunda.

show more

Share/Embed