Tiwadziwe: Dyson Gonthi
TIMVENI TV TIMVENI TV
1.19K subscribers
14,978 views
127

 Published On Premiered Aug 12, 2024

M'modzi mwa anthu olimbikitsa chikhalidwe komanso katswiri pa masewero, Dyson Gonthi kukambapo makhalidwe abwino omwe achinyamata angatengere pomwe dziko likusintha.

Onerani program ya Tiwadziwe lolemba lilironse pa Timveni Online Official Facebook Page kuyambira 12:00.
#Tiwadziwe #Timveni #tvshow24h #tv

show more

Share/Embed